Mawu a M'munsi
a Pa nthawi imene dzikoli linkalamuliridwa ndi boma lachikomyunizimu, Mabaibulo ankasowa kwambiri. Izi zinkachitika ngakhale kuti mabuku ena a m’Baibulo anali atamasuliridwa kale m’Chijojiya. Mabukuwa anamasuliridwa m’zaka za m’ma 400 C.E.—Onani bokosi la mutu wakuti, “Baibulo la M’Chijojiya.”