Mawu a M'munsi
a Ulosi wa m’Baibulo komanso mmene zinthu zili padzikoli zimasonyeza kuti tikukhala ‘m’masiku otsiriza’ ndipo nthawi imeneyi ndi “yovuta.” (2 Timoteyo 3:1) Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani yakuti “Kodi Chizindikiro cha ‘Masiku Otsiriza’ Kapena Kuti ‘Nthawi ya Mapeto’ N’chiyani?”