Mawu a M'munsi a M’nkhaniyi mawu akuti “nkhawa” sakugwiritsidwa ntchito ponena za matenda ovutika maganizo koma akuimira nkhawa zomwe munthu amatha kukhala nazo tsiku lililonse. Amene akudwala matenda ovutika maganizo angachite bwino kukaonana ndi adokotala.—Luka 5:31.