Mawu a M'munsi
a “Wotchi yongoyerekezera yosonyeza nthawi yakutha kwa dziko inakonzedwa kuti izichenjeza anthu za kufupika kwa nthawi yoti dzikoli lithe chifukwa cha zida zoopsa zamakono zimene anthu akupanga. Limeneli ndi chenjezo lothandiza anthu kudziwa kuti akuyenera kupeza njira zothetsera mavuto n’cholinga choti dzikoli lisathe.”—Bulletin of the Atomic Scientists.