Mawu a M'munsi
a Buku lina lotanthauzira mawu a m’Baibulo linamasulira mawu akuti “phompho” kuti ndi dzenje lopanda malire. (Vine’s Expository Dictionary of Old and New Testament Words) Pomwe Baibulo la King James Version linamasulira kuti “dzenje lopanda pothera.” Koma Baibulo likamanena za mawu amenewa limakhala likutanthauza malo amene chinthu sichingathe kuchita chilichonse.