Mawu a M'munsi
a Ulendo wa nambala 4, mawuwa amapezeka m’Baibulo la King James Version pa Chivumbulutso 1:11. Komabe m’Mabaibulo ambiri, pavesili palibe mawu amenewa chifukwa sapezeka m’Baibulo loyambirira la Chigiriki. Patapita nthawi, m’pamene mawu amenewa anadzayamba kupezeka pavesili m’malemba opatulika.