Mawu a M'munsi
a Nkhani zikuluzikulu ngati zimenezi zimafunika kuzikambirana musanakwatirane. Komabe nthawi zina zinthu zikhoza kusintha mosayembekezereka, kapenanso nthawi ikamapita wina akhoza kusintha maganizo amene anali nawo poyamba.—Mlaliki 9:11.