Mawu a M'munsi
a Dipatimenti Yoyang’anira Sukulu Zophunzitsa Atumiki a Mulungu ndi imene imakonza maphunzirowa motsogoleredwa ndi Komiti Yoona za Ntchito Yophunzitsa ya Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova. Alangizi ochokera m’dipatimentiyi ndi amene amaphunzitsa sukuluyi limodzi ndi alangizi ena kuphatikizapo abale a m’Bungwe Lolamulira.