Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zoonera ndi Zomvetsera Zithunzi komanso mavidiyo zopezeka pamalowa, zimakonzedwa patachitika kafukufuku wokwanira. Pa zinthu zingapo zomwe angakonze, nthawi zina okonza zithunzi ndi mavidiyowa angasankhe kuika chithunzi kapena vidiyo imodzi.