No. 1 Kodi Tingadzakhaledi Otetezeka Padzikoli? Zimene Zili M’magaziniyi MAVUTO AMENE TIKUKUMANA NAWO Zomwe Zikuchititsa kuti Tisakhale Otetezeka CHIFUKWA CHAKE TIKULEPHERA KUTHANA NDI MAVUTO Kudziwa Chimene Chikuyambitsa Mavuto ZOMWE ZIKUCHITIKA POLIMBANA NDI MAVUTO Maphunziro Okhudza Makhalidwe Abwino ZOMWE ANACHITA POLIMBANA NDI MAVUTO Nkhani ya Ricardo ndi Andres BOMA LIMENE LIDZATHETSE MAVUTO “Ndipo Mtendere Sudzatha” MMENE MAVUTO ONSE ADZATHERE Ufumu wa Mulungu Ukamadzalamulira “Padzakhala Mtendere Wochuluka” Kodi Munayamba Mwadzifunsapo?