March Magazini Yophunzira Zimene Zili M’magaziniyi NKHANI YOPHUNZIRA 9 Kodi Achinyamata Mungatani Kuti Anthu Ena Azikudalirani? NKHANI YOPHUNZIRA 10 Aliyense Mumpingo Angathandize Ophunzira Baibulo Kuti Abatizidwe NKHANI YOPHUNZIRA 11 Malemba Angatithandize Kuti Tizipirira NKHANI YOPHUNZIRA 12 Chikondi Chimatithandiza Kupirira Ena Akamadana Nafe NKHANI YOPHUNZIRA 13 Kodi Yehova Amatiteteza Bwanji? Mafunso Ochokera Kwa Owerenga Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG