February Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya February 2020 Zimene Tinganene February 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 12-14 Pangano Lomwe Limakukhudzani MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tingaphunzire Chiyani Kuchokera mu Nyimbo za Broadcasting? February 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 15-17 N’chifukwa chiyani Yehova anasintha dzina la Abulamu ndi Sarai? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zimene Mwamuna ndi Mkazi Wake Angachite Kuti Alimbitse Chikondi M’banja Lawo February 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 18-19 “Woweruza wa Dziko Lonse Lapansi” Anawononga Sodomu ndi Gomora MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumapindula ndi Kabuku ka Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku? February 24–March 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 20-21 Yehova Amakwaniritsa Zomwe Walonjeza