December Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya December 2017 Zitsanzo za Ulaliki December 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ZEPHANIYA 1–HAGAI 2 Funafunani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike December 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ZEKARIYA 1-8 ‘Gwirani Chovala cha Munthu Amene ndi Myuda’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzilalikira Munthu Aliyense wa M’gawo Lanu December 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ZEKARIYA 9-14 Musachoke ‘M’chigwa cha Pakati pa Mapiri’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mbali Yatsopano pa Misonkhano ya Mkati mwa Mlungu December 25-31 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALAKI 1-4 Kodi Ukwati Wanu Umakondweretsa Yehova? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Chikondi Chenicheni