September Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 2018 Zimene Tinganene September 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 1-2 Chozizwitsa Choyamba cha Yesu September 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 3-4 Yesu Analalikira Mayi Wachisamariya MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Mmene Mungayambire Kucheza ndi Anthu Kuti Muwalalikire Mwamwayi September 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 5-6 Muzitsatira Yesu Muli ndi Zolinga Zabwino MOYO WATHU WACHIKHRISTU Sipanawonongeke Chilichonse September 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 7-8 Yesu Ankalemekeza Atate Wake MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzitsanzira Khristu pa Nkhani Yokhala Odzichepetsa Komanso Kuzindikira Malire Anu