12 Ndalama, Kulemera kwa Zinthu, Miyezo
Miyezo imene ili m’munsiyi ndi maavereji amene akuchokera m’maumboni a m’Baibulo ndi zimene ofukula m’mabwinja anapeza. Miyezo yonse yamakono imene tagwiritsa ntchito pano si yofanana ndendende ndi miyezo yakale.
TCHATI CHOSONYEZA KULEMERA KWA NDALAMA ZIMENE ANAGWIRITSA NTCHITO M’MALEMBA ACHIHEBERI
Muyezo Wamakono |
||
Gera imodzi |
= 1⁄20 ya sekeli |
= Magalamu 0.57 |
Beka imodzi (hafu ya sekeli) |
= Magera 10 |
= Magalamu 5.7 |
Sekeli imodzi |
= Mabeka 2 |
= Magalamu 11.4 |
Mina (mane) imodzi |
= Masekeli 50 |
= Magalamu 570 |
Talente imodzi |
= Ma mina 60 |
= Makilogalamu 34.2 |
Dariki imodzi (ya ku Perisiya, yagolide) |
= Magalamu 8.4 |
|
Dariki imodzi (ya ku Perisiya, yasiliva) (yotchedwanso kuti sekeli) |
= Magalamu 5.60 |
TCHATI CHOSONYEZA KULEMERA KWA NDALAMA ZA AGIRIKI NDI AROMA M’MALEMBA ACHIGIRIKI
Muyezo Wamakono |
||
Dinari imodzi (ya Aroma, yasiliva) |
= Magalamu 3.85 |
|
Dirakima imodzi (ya Agiriki, yasiliva) |
= Magalamu 3.40 |
|
Siteta imodzi (yasiliva) |
= Madirakima 4 |
= Magalamu 13.6 |
Mina imodzi |
= Madirakima 100 |
= Magalamu 340 |
Talente imodzi (golide kapena siliva) |
= Ma mina 60 |
= Makilogalamu 20.4 |
MUYEZO WA ZINTHU ZAMADZI
Hini imodzi |
= Malita 3.67 |
|
Mtsuko umodzi |
= Mahini 6 |
= Malita 22 |
Kori imodzia |
= Mitsuko 10 |
= Malita 220 |
MUYEZO WA ZINTHU ZOMWE SI ZAMADZI
Omeri imodzi |
= Malita 2.2 |
|
Seya imodzi |
= 3 1⁄3 ya omeri |
= Malita 7.33 |
Efa imodzi |
= Maseya 3 |
= Malita 22 |
Homeri imodzi (korali) |
= Maefa 10 |
= Malita 220 |
MIYEZO YOYEZERA MTUNDA
Mphipi imodzi ya chala |
= 1⁄4 ya chikhatho |
= Masentimita 1.85 |
Chikhatho chimodzi |
= Mphipi ya zala 4 |
= Masentimita 7.4 |
Chikhatho chimodzib |
= Zikhatho 3 |
= Masentimita 22.2 |
Mkono umodzi |
= Zikhatho 2 |
= Masentimita 44.5 |
Mkono umodzi wautalic |
= Zikhatho 7 |
= Masentimita 51.8 |
Bango limodzi |
= Mikono 6 |
= Mamita 2.67 |
Bango limodzi lalitali |
= Mikono yaitali 6 |
= Mamita 3.116 |
a Umenewu unalinso muyezo wa zinthu zomwe si zamadzi wofanana ndi muyezo wa homeri.
b Chikhatho ichi n’chosiyana ndi chikhatho cha masentimita 7.4 chimene chili pamwambapa. Onani mawu a m’munsi pa Eks 28:16.
c N’kutheka kuti umenewu unali wofanana ndi muyeso wa mkono “wakale” wotchulidwa pa 2Mbi 3:3.