14 Zovala za Mkulu wa Ansembe
(Onani m’Baibulo lenileni kuti mumvetse izi)
Mwala wa Onekisi
Matcheni
Chovala Pachifuwa Chachiweruzo
Miyala 12 Yamtengo Wapatali
Nduwira
Chizindikiro Chopatulika cha Kudzipereka
Mkanjo Wansalu Wamandalasi
Lamba Womangira Efodi
Efodi
Malaya a Buluu Odula Manja
Mpendero Wokhala ndi Mabelu ndi Makangaza