Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maholide
    Kukambitsirana za m’Malemba
    • 1 Yoh. 5:19: “Dziko lonse lapansi ligona mwa woipayo.” (Yerekezerani ndi Yohane 14:30; Chivumbulutso 13:1, 2; Danieli 2:44.)

      Maholide ena a m’malowo ndi amtundu

      Ngochuluka. Sangakambitsiridwe onse panopa. Koma chidziŵitso cha m’mbiri choperekedwa pamwambapa chimasonyeza zimene ziyenera kupendedwa paholide iriyonse, ndipo malamulo a makhalidwe abwino Abaibulo amene afotokozedwa kale amapereka chitsogozo chokwanira kwa awo amene chikhumbo chawo chachikulu chiri kuchita zokondweretsa kwa Yehova Mulungu.

  • Maloto
    Kukambitsirana za m’Malemba
    • Maloto

      Tanthauzo: Maganizo kapena zithunzi zamaganizo za munthu m’nthaŵi ya kugona. Baibulo limatchula maloto wamba, maloto ochokera kwa Mulungu, ndi maloto ophatikizapo kuombeza.—Yobu 20:8; Num. 12:6; Zek. 10:2.

      Kodi maloto m’nthaŵi yathu ali ndi tanthauzo lapadera?

      Kodi nchiyani chimene ofufuza apeza ponena za maloto?

      “Munthu aliyense amalota,” ikutero The World Book Encyclopedia (1984, Vol. 5, p. 279). “Achikulire ambiri amalota pafupifupi mphindi 100 mkati mwa tulo ta maora asanu ndi atatu.” Chotero maloto ali chokumana nacho chozoloŵereka cha anthu.

      Dr. Allan Hobson, wa ku Harvard Medical School anati: “Ali chochitika chosatsimikizirika chimene chingatathauziridwe mwanjira iriyonse imene wotanthauzirayo wakhotererako. Koma tanthauzo lawo liri kwa munthu wolotayo—osati m’loto lenilenilo.” Posimba mfundoyi, “Science Times” chigawo cha The New York Times inawonjezera kuti: “M’masukulu amene amaika chigogomezero chachikulu pamaloto, muli njira zambiri zopezera tanthauzo lamaganizo la maloto, iriyonse ikumasonyeza mipangidwe ya nthanthi zosiyanasiyana. Wotsatira njira ya Freud adzapeza tanthauzo la mtundu wakuti m’loto, pamene wotsatira Jungi adzapeza lina ndipo Mgestalt womasulira maloto

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena