-
Chigawo 1Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 1
Mulungu amalankhula nafe kudzera m’Baibulo. 2 Timoteyo 3:16
Anthu kulikonse akumvetsera. Mateyu 28:19
-
-
Chigawo 2Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 2
Yehova analenga chilichonse kumwamba . . . ndi padziko lapansi. Salimo 83:18; Chivumbulutso 4:11
-
-
Chigawo 3Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 3
Yehova anapatsa Adamu ndi Hava zinthu zabwino zambiri. Genesis 1:28
Mulungu anawauza kuti asadye chipatso cha mtengo umodzi. Genesis 2:16, 17
-
-
Chigawo 4Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 4
Adamu ndi Hava sanamvere Mulungu, choncho anafa. Genesis 3:6, 23
Akufa sadziwa chilichonse, amangokhala ngati fumbi. Genesis 3:19
-
-
Chigawo 5Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 5
Anthu ambiri m’nthawi ya Nowa ankachita zoipa. Genesis 6:5
Nowa anamvera Mulungu ndipo anapanga chingalawa. Genesis 6:13, 14, 18, 19, 22
-
-
Chigawo 6Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 6
Mulungu anawononga anthu oipa, koma anapulumutsa Nowa ndi banja lake. Genesis 7:11, 12, 23
Posachedwapa, Mulungu awononganso oipa ndi kupulumutsa anthu abwino. Mateyu 24:37-39
-
-
Chigawo 7Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 7
Yehova anatumiza Yesu padziko lapansi. 1 Yohane 4:9
Yesu ankachita zinthu zabwino koma anthu ankadana naye. 1 Petulo 2:21-24
-
-
Chigawo 8Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 8
Yesu anatifera kuti tipeze moyo. Yohane 3:16
Mulungu anaukitsa Yesu ndipo anamuika kukhala Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Danieli 7:13, 14
-
-
Chigawo 9Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 9
Mavuto amene tikukumana nawo padziko lapansi akusonyeza kuti Ufumu wa Mulungu uli pafupi. Luka 21:10, 11; 2 Timoteyo 3:1-5
Ufumuwo udzachotsa zoipa zonse. 2 Petulo 3:13
-
-
Chigawo 10Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 10
Ambiri mwa anthu amene anamwalira adzaukitsidwa padziko lapansi. Machitidwe 24:15
Ufumu wa Mulungu udzathetsa mavuto onse. Chivumbulutso 21:3, 4
-
-
Chigawo 11Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 11
Mulungu amamvetsera mapemphero athu. 1 Petulo 3:12
Tingatchule zinthu zosiyanasiyana popemphera. 1 Yohane 5:14
-
-
Chigawo 12Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 12
Chikondi n’chofunika kwambiri kuti aliyense m’banja akhale wosangalala. Aefeso 5:33
Khalani okoma mtima ndiponso okhulupirika, osati ankhanza. Akolose 3:5, 8-10
-
-
Chigawo 13Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 13
Muzipewa kuchita zinthu zoipa. 1 Akorinto 6:9, 10
Muzichita zinthu zabwino. Mateyu 7:12
-
-
Chigawo 14Mverani Mulungu
-
-
Chigawo 14
Khalani kumbali ya Mulungu. 1 Petulo 5:6-9
Sankhani mwanzeru, mverani Mulungu. Mateyu 7:24, 25
-