Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Muzilankhula Mawu “Olimbikitsa”
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
    • N’CHIFUKWA CHIYANI TIYENERA KUSAMALA POLANKHULA?

      4, 5. Kodi miyambi ina ya m’Baibulo imafotokoza kuti mawu ali ndi mphamvu yotani?

      4 Chifukwa chimodzi chofunika kwambiri chomwe tiyenera kukhalira osamala polankhula n’chakuti mawu ali ndi mphamvu. Lemba la Miyambo 15:4 limati: “Lilime lodekha lili ngati mtengo wa moyo, koma lilime lachinyengo limapweteketsa mtima.”a Mawu odekha amalimbikitsa ena monga mmene madzi amapangitsira mtengo umene unafota kusangalala. Mosiyana ndi zimenezo, mawu oipa a lilime lachinyengo amakhumudwitsa ena. Zoonadi, zolankhula zathu zingavulaze kapena kuchiritsa ena.—Miyambo 18:21.

  • Muzilankhula Mawu “Olimbikitsa”
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
    • a Mawu a Chiheberi amene anawamasulira kuti ‘chinyengo’ pa Miyambo 15:4 angatanthauzenso ‘kukhota’ kapena ‘kupotoka.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena