-
Mfundo Zazikulu za Nyimbo ya SolomoNsanja ya Olonda—2006 | November 15
-
-
2:7; 3:5—N’chifukwa chiyani mtsikanayo akulumbirira akazi akumpanda wa mfumu pogwiritsa ntchito “mphoyo, ndi nswala ya kuthengo”? Mphoyo ndi nswala zili ndi maonekedwe ake ochititsa kaso ndiponso okongola kwambiri. Kwenikweni, Msulamiyu, akulumbirira akazi akumpanda wa mfumu kuti chilichonse chimene chili chochititsa kaso ndiponso chokongola chisautse chikondi mwa iye.
-
-
Mfundo Zazikulu za Nyimbo ya SolomoNsanja ya Olonda—2006 | November 15
-
-
2:7; 3:5. Mtsikana wakumudzi ameneyu sanakopeke ndi Solomo. Komanso analumbirira akazi akumpanda wa mfumu kuti asayese kuutsa chikondi mwa iye kaamba ka aliyense kupatulapo m’busayo. N’kosatheka ndiponso kosayenera kwa munthu kukonda mwamuna kapena mkazi aliyense. Mkhristu amene akufuna mnzake woti akwatirane naye, ayenera kusankha mtumiki wokhulupirika wa Yehova basi.—1 Akorinto 7:39.
-