Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Nkhosazo ndi Mbuzizo Zili ndi Mtsogolo Motani?
    Nsanja ya Olonda—1995 | October 15
    • 4. Kodi fanizo la nkhosa ndi mbuzi likuyamba ndi mawu otani ponena za Yesu, ndipo ndaninso amene akutchulidwa?

      4 Yesu akuyamba fanizo lake mwakuti: “Koma pamene Mwana wa munthu adzadza.” Mwachionekere mukumdziŵa “Mwana wa munthu.” Kaŵirikaŵiri olemba Mauthenga Abwino anagwiritsira ntchito mawuwo kunena Yesu. Ngakhale Yesu mwiniyo anatero, mosakayika akumakumbuka masomphenya a Danieli a “wina ngati mwana wa munthu” akuyandikira kwa Nkhalamba ya Kale Lomwe kulandira “ulamuliro ndi ulemerero, ndi ufumu.” (Danieli 7:13, 14; Mateyu 26:63, 64; Marko 14:61, 62) Pamene Yesu ndiye munthu wamkulu m’fanizoli, iye saali yekha. Poyambirira m’nkhaniyo, monga momwe pakufotokozera pa Mateyu 24:30, 31, iye anati pamene Mwana wa munthu ‘alinkudza ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu,’ angelo ake adzachita mbali yofunika kwambiri. Mofanana ndi zimenezo, fanizo la nkhosa ndi mbuzi likusonyeza angelo pamodzi ndi Yesu pamene iye ‘akukhala pa chimpando cha kuŵala kwake’ kuweruza. (Yerekezerani ndi Mateyu 16:27.) Koma Woweruzayo ndi angelo ake ali kumwamba, choncho kodi fanizolo likufotoza za anthu?

  • Kodi Nkhosazo ndi Mbuzizo Zili ndi Mtsogolo Motani?
    Nsanja ya Olonda—1995 | October 15
    • Adza ndi ulemerero waukulu Afika mu ulemerero ndi kukhala

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena