Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Pitirizani Kuchita Zinthu Mogwirizana Mumpingo
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
    • 3. Kodi muyenera kuchita chiyani mukasemphana maganizo ndi Mkhristu mnzanu?

      Ngakhale kuti ndife anthu ogwirizana, timasemphana maganizo kapena kukhumudwitsana chifukwa chakuti ndife anthu ochimwa. Choncho, Mawu a Mulungu amatiuza kuti: “Pitirizani . . . kukhululukirana ndi mtima wonse . . . monga Yehova anakukhululukirani ndi mtima wonse, inunso teroni.” (Werengani Akolose 3:13.) Anthufe timakhumudwitsa Yehova kambirimbiri komabe iye amatikhululukira. Choncho iye amafuna kuti nafenso tizikhululukira abale ndi alongo athu. Mukazindikira kuti mwakhumudwitsa winawake, inuyo muziyesetsa kukambirana ndi mnzanuyo n’cholinga choti muthetse kusamvana.​—Werengani Mateyu 5:23, 24b

  • Pitirizani Kuchita Zinthu Mogwirizana Mumpingo
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
    • Nthawi zina nafenso timakhumudwitsa ena. Ndiye tizitani zimenezi zikachitika? Onerani VIDIYO, kenako mukambirane funso lotsatirali.

      VIDIYO: Kukhazikitsa Mtendere Kumabweretsa Madalitso (6:01)

      • Kodi mlongo wamuvidiyoyi anachita zotani kuti akhazikitse mtendere?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena