Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Anawakonzekeretsa Kuti Azilalikira Ngakhale Pamene Akuzunzidwa
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
    • Chifukwa chakuti ntchito yolalikira inali yofunika kwambiri, Yesu anauza otsatira akewo kuti ayenera kukhala osamala kuti akwanitse kugwira ntchitoyi. Iye ananena kuti: “Akakuzunzani mumzinda wina, muthawire mumzinda wina, pakuti ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike.”—Mateyu 10:23.

  • Anawakonzekeretsa Kuti Azilalikira Ngakhale Pamene Akuzunzidwa
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
    • Choncho, n’zoonekeratu kuti pamene Yesu ankapereka malangizo amenewa kwa atumwi ake ankanena zimene zidzachitike m’tsogolo. Kumbukiraninso kuti anauza ophunzira ake kuti sadzamaliza kuzungulira mizinda yonse akugwira ntchito yolalikirayi “Mwana wa munthu asanafike.” Ponena mawu amenewa Yesu ankatanthauza kuti ophunzira ake sadzamaliza kulalikira za Ufumu wa Mulungu, Yesu Khristu yemwe ndi Mfumu asanabwere monga woweruza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena