Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mwini Chuma ndi Lazaro Akumana ndi Kusintha
    Nsanja ya Olonda—1989 | April 1
    • “Ndipo kunali kuti,” Yesu akutero, “wopemphayo adafa, ndi kuti anatengedwa iye ndi angelo kunka ku chifuwa cha Abrahamu; ndipo mwini chumayo adafanso, naikidwa m’manda. Ndipo m’Hade anakweza maso ake, pokhala nawo mazunzo, nawona Abrahamu patali, ndi Lazaro m’chifuwa mwake.”

  • Mwini Chuma ndi Lazaro Akumana ndi Kusintha
    Nsanja ya Olonda—1989 | April 1
    • Awo a gulu lodzichepetsa la Lazaro, wolapa akufa ku mkhalidwe wawo wakale womanidwa mwauzimu ndi kukhala m’malo a chiyanjo chaumulungu. Pamene kuli kwakuti kale iwo anayang’ana kwa atsogoleri achipembedzo kaamba ka zochepera zomwe zinagwa kuchokera pa gome lauzimu, tsopano chowonadi cha m’Malemba choperekedwa ndi Yesu chikudzaza zosowa zawo. Iwo mwakutero akubweretsedwa m’chifuwa, kapena m’malo oyanjidwa, a Abrahamu Wamkulu, Yehova Mulungu.

      Ku mbali ina, awo omwe akupanga gulu la mwini chumalo akubwera pansi pa kupanda chiyanjo chaumulungu chifukwa cha kukana mowumirira kulandira uthenga wa Ufumu wophunzitsidwa ndi Yesu. Iwo mwakutero akufa ku mkhalidwe wawo wakale wowoneka wachiyanjo. M’chenicheni, iwo akulankhulidwa kukhala m’chizunzo chophiphiritsira. Mvetserani pamene mwini chumayo akulankhula:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena