Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yerusalemu ndi Kachisi Amene Yesu Ankamudziŵa
    ‘Onani Dziko Lokoma’
    • Yesu nthaŵi zambiri anali kukacheza kwa mabwenzi ake Lazaro, Mariya, ndi Marita ku Betaniya, “pafupifupi makilomita atatu” kum’maŵa kwa Yerusalemu. (Yoh. 11:1, 18, NW, mawu a m’munsi; 12:1-11; Luka 10:38-42; 19:29; onani “Dera la Yerusalemu,” patsamba 18.) Patatsala masiku ochepa kuti aphedwe, Yesu anafika ku Yerusalemu podutsira ku Phiri la Azitona. Tangoyerekezerani kuti mukumuona akuima ndi kuyang’ana kumadzulo pa mzindawo, n’kumaulirira. (Luka 19:37-44) Zimene iye anaona zingakhale zofanana ndi zimene mukuona patsamba lotsatirali pamwamba. Kenako Yesu analoŵa m’Yerusalemu atakwera pabulu, ndipo ayenera kuti analoŵera pa chimodzi mwa zipata za kum’maŵa kwa mzindawo. Makamu a anthu anam’tamanda monga Mfumu ya Israyeli ya m’tsogolo.—Mat. 21:9-12.

  • Yerusalemu ndi Kachisi Amene Yesu Ankamudziŵa
    ‘Onani Dziko Lokoma’
    • CHIGWA CHA HINOMU (GEHENA)

      [Zithunzi patsamba 30]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena