-
Yerusalemu ndi Kachisi Amene Yesu Ankamudziŵa‘Onani Dziko Lokoma’
-
-
Kumpoto kwa kachisiyo, pathamanda la Betesda, Yesu anachiritsa munthu yemwe anadwala zaka 38. Mwana wa Mulungu ameneyu anachiritsanso munthu wakhungu, yemwe anamuuza kuti akasambe m’thamanda la Siloamu lomwe linali kum’mwera kwa mzindawo.—Yoh. 5:1-15; 9:1, 7, 11.
-
-
Yerusalemu ndi Kachisi Amene Yesu Ankamudziŵa‘Onani Dziko Lokoma’
-
-
Nyumba ya Kazembe
-