Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • “Anapitiriza kufalikira Ndipo Sankagonjetseka” Ngakhale Kuti Panali Otsutsa
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
    • 13, 14. (a) Kodi Yehova anathandiza Paulo kuti achite chiyani? (b) Kodi ana a Sikeva anachita zinthu ziti zolakwika, nanga masiku ano anthu ambiri a m’matchalitchi amene amati ndi a Chikhristu amachitanso zinthu ziti zolakwika zofanana ndi zimenezi?

      13 Luka akutiuza kuti panali zinthu zabwino kwambiri zimene zinachitika pa utumiki wa Paulo chifukwa Yehova anamuthandiza “kuchita zinthu zamphamvu komanso zodabwitsa.” Anthu ankatenga ngakhale tinsalu ndi maepuloni amene Paulo ankavala n’kupita nazo kwa anthu odwala ndipo ankachiritsidwa. Komanso anthu ankatulutsa mizimu yoipa pogwiritsa ntchito zinthu zimenezi.c (Mac. 19:11, 12, mawu a m’munsi.) Anthu ambiri anachita chidwi ndi zozizwitsa zimenezi, zomwe zinasonyeza kuti Satana wagonjetsedwa. Koma si onse amene ankasangalala nazo.

  • “Anapitiriza kufalikira Ndipo Sankagonjetseka” Ngakhale Kuti Panali Otsutsa
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
    • c N’kutheka kuti timeneti tinali tinsalu timene Paulo ankamanga pachipumi kuti thukuta lisamayenderere n’kulowa m’maso. Komanso mfundo yakuti Paulo ankavala maepuloni ikusonyeza kuti iye ankagwira ntchito yake yokonza matenti pa nthawi yake yopuma, mwina m’mawa kwambiri.​—Mac. 20:34, 35.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena