Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • “Anapitiriza Kukhala Osangalala Komanso Mzimu Woyera Unkawathandiza Kwambiri”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
    • 2 Zaka 14 m’mbuyomo, Yesu anali atauza otsatira ake kuti: “Mudzakhala mboni zanga mu Yerusalemu, ku Yudeya konse ndi ku Samariya, mpaka kumalekezero a dziko lapansi.” (Mac. 1:8) Kusankhidwa kwa Baranaba ndi Saulo kuti akhale amishonale kunathandiza kuti ulosi wa Yesu ukwaniritsidwe.b

  • “Anapitiriza Kukhala Osangalala Komanso Mzimu Woyera Unkawathandiza Kwambiri”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
    • b Pa nthawiyi, mipingo inkapezeka m’madera akutali monga ku Antiokeya wa ku Siriya, mzinda omwe unali pa mtunda wa makilomita pafupifupi 550 kumpoto kwa Yerusalemu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena