Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsamba 5
  • “Ndikudziwa Ntchito Zako”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ndikudziwa Ntchito Zako”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kuulula Chinsinsi Chopatulika
    Mapeto Osangalatsa a Masomphenya a M’buku la Chivumbulutso
  • Kristu Amatsogolera Mpingo Wake
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Utsogoleri Wokangalika wa Kristu Lerolino
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Kodi Mpingo wa Chikhristu Umayendetsedwa bwanji?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 November tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 1-3

“Ndikudziwa Ntchito Zako”

1:20; 2:1, 2

  • Abale awiri akukambirana ndi m’bale wina; dzanja la Yesu lili ndi nyenyezi 7

    “Nyenyezi 7”: Odzozedwa omwe ndi akulu komanso zingatanthauze akulu ena onse

  • “M’dzanja [la Yesu] lamanja”: Yesu ali ndi udindo wotsogolera komanso kuchita chilichonse ndi nyenyezi zimenezi. Ngati mkulu wina sakuchita bwino, Yesu amadziwa njira komanso nthawi yoyenera kumuthandizira

  • “Zoikapo nyale 7 zagolide”: Mpingo wachikhristu. M’chihema, zoikapo nyale zinkathandiza kuti kuwala kwa nyale kuzionekera. Mpingo wachikhristu nawonso umathandiza kuti kuwala kwa choonadi kuzionekera. (Mat. 5:14) Ndiponso Yesu ‘amayenda’ pakati pa zoikapo nyale m’njira yakuti iye amayang’anira ntchito zomwe zimachitika m’mipingo yonse

Kodi mfundo za m’masomphenyawa zingakuthandizeni bwanji . . .

  • akulu akamakupatsani malangizo kapena uphungu?

  • mukamaona zopanda chilungamo komanso mavuto ena mumpingo wanu?

  • kuti muzilalikira uthenga wabwino pa nthawi iliyonse?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena