Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 55
  • Tidzapeza Moyo Wosatha!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tidzapeza Moyo Wosatha!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tidzakhala Ndi Moyo Wosatha
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 55

Nyimbo 55

Tidzapeza Moyo Wosatha!

Losindikizidwa

(Yohane 3:16)

1. Onani m’maganizo

Anthuwo pamtendere

Zosautsa zathadi!

Palibe kulira.

(KOLASI)

Imbani mokondwa!

Ngakhale inunso

Patsikulo mudzati,

“Moyo wosathadi!”

2. Anthunso Okalamba

Adzakhala ’nyamata.

Mavutowa adzatha,

Anthu sadzalira.

(KOLASI)

Imbani mokondwa!

Ngakhale inunso

Patsikulo mudzati,

“Moyo wosathadi!”

3. Anthu’fe tidzakondwa

Poimbira Mulungu.

Nthawi zonse tidzati,

“Zikomo Yehova.”

(KOLASI)

Imbani mokondwa!

Ngakhale inunso

Patsikulo mudzati,

“Moyo wosathadi!”

(Onaninso Yobu 33:25; Sal. 72:7; Chiv. 21:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena