Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 109
  • Moyo Wosatha Ulonjezedwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Moyo Wosatha Ulonjezedwa
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
    Imbirani Yehova
  • Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Lonjezo la Mulungu la Paradaiso
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 109

Nyimbo 109

Moyo Wosatha Ulonjezedwa

(Salmo 37:29)

1. Moyo ulonjezedwadi

Ndi Mulungu wamkulu,

Pansi pano muungwiro.

Sikulota ndithu.

(Korasi)

2. Lonjezo la Ya n’lowona

Lidzakwaniritsidwa:

‘Ofatsa adzakondwera.’

Ndi chifuno cha Ya.

(Korasi)

3. Mulungu watsimikiza

Kuchita zatsopano.

Madalitso adzachoka

M’mwamba monga mame.

(Korasi)

4. Yesu anatsimikiza,

Paradaiso adza.

M’dziko latsopano M’lungu

Adzalambiridwa.

(KORASi)

Tingapeze moyo.

Tiyeseyesetse.

Ya ngwodalirika.

Ali wowona.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena