Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 133
  • Kufesa Mbewu za Ufumu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kufesa Mbewu za Ufumu
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Fesani Mbewu za Ufumu
    Imbirani Yehova
  • ‘Khalanibe M’mawu Anga’
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Tizifesa Mbewu za Ufumu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • ‘Mulungu Ndi Amene Amakulitsa’!
    Nsanja ya Olonda—2008
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 133

Nyimbo 133

Kufesa Mbewu za Ufumu

(Mateyu 13:4-8, 19-23)

1. Idzani akapolo a Yehova

Mwadzipereka kwa M’lungu.

Kuntchito yoikizidwa kwa inu;

Yendani monga Kristuyo.

Muli ndi ntchito yofesa cho’nadi

Panthaka yoberekayo

Zipatso zabwino ngati muchita

Utumiki mokwaniratu.

2. Zina zidzagwera m’mbali mwa njira,

Koma mbalame zidzadya;

Pamene zina zigwera pamwala,

Nkufota ndi kutenthako.

Nkhaŵa ndi dyera ziri zonga minga

Yotsamwitsa mbewu zanu.

Komabe zina zingagwere pansi

Pamalo abwino oyera.

3. Kuti zigwere panthaka yabwino

Zimadalira pa inu.

Mwa kuleza mtima ndi mwachikondi,

Mungaingitse “mbalame.”

Pokhala maso muchotsetu minga,

Mungayembekezeretu

Kuti mutute makumi atatu

Ngakhaletu zana limodzi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena