Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 46
  • Malemba—Ouziridwa ndi Opindulitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Malemba—Ouziridwa ndi Opindulitsa
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Malemba Anauziridwa ndi Mulungu
    Imbirani Yehova
  • Malemba Anauziridwa Ndi Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Mawu a Mulungu Azikuthandizani Ndipo Muzithandiza Nawo Ena
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Chilango Chimabala Chipatso cha Mtendere
    Nsanja ya Olonda—1987
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 46

Nyimbo 46

Malemba—Ouziridwa ndi Opindulitsa

(2 Timoteo 3:16, 17)

1. Mawu a Ya ndinyali,

Yotsogoza mumdima.

Muuni wa ufulu;

‘Cho’nadi chimasula.’

2. Mwa Malemba awatu,

Tazindikira M’lungu.

Kudalira mwa iwo,

Tidzafupidwa moyo.

3. Mawu ngouziridwa,

Amatiphunzitsatu.

Amawongola zinthu,

Ndi uphungu wa M’lungu.

4. Ndiopindulitsatu,

Apatsa chilangizo;

Kuti munthu wa M’lungu

Akhale wokonzeka.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena