-
Chikhulupiriro Chathu Chimatilimbikitsa Kuchita Ntchito ZabwinoUtumiki wa Ufumu—2002 | May
-
-
1 Chikhulupiriro chinachititsa Nowa, Mose, ndi Rahabi kuchita kanthu kenakake. Nowa anamanga chingalawa. Mose anakana kusangalala kwanthaŵi yochepa m’nyumba ya Farao. Rahabi anabisa azondi ndipo kenako anamvera malangizo awo, zimene zinapulumutsa banja lake. (Aheb. 11:7, 24-26, 31) Kodi chikhulupiriro chathu lerolino chikutilimbikitsa kuchita ntchito zabwino zotani?
-
-
Kodi Mukugwiritsa Ntchito Bulosha la Mulungu Amafunanji Kuyambitsira Maphunziro?Utumiki wa Ufumu—2002 | May
-
-
1 Kodi mukudziŵa kuti kukambirana mokhazikika ndiponso mwadongosolo, ngakhale mwachidule, ndi munthu wachidwi nkhani za m’Baibulo zimene zili m’buku lina lililonse loyenera lothandiza kuphunzira Baibulo, ndiye kuti mukuchititsa phunziro la Baibulo? Inde, limenelo ndi phunziro la Baibulo kaya mukuchitira pa nkhonde kapena pa telefoni. Bwanji osayesetsa m’miyezi ya May ndi June kuyambitsa phunziro lotereli pogwiritsa ntchito bulosha la Mulungu Amafunanji?
-