Nyimbo 136
Olambira Okhulupirika Alemekeza Yehova
1. Okhulupirika, akutamandani;
Chotero, dzetsani chipambano.
Tikutamandeni; Muli wolungama.
Timachita ntchito mowonadi.
2. Tilemekeza’nu—tikuthokozani—
Tisamale zonse, ndi chiyero.
Chonde tidziŵetu chikhulupiliro.
Mbuye tisonyeze umphumphuwo.
3. Tidziŵitseni za Ufumu wanuwo
Mumachirikiza mwapamwamba.
Sonyani ubwino, kuti asagwedi.
Mutimve kupempha, mosaleka.
4. Tate m’tithandize, kugonjetsa mantha,
Ponena Ufumu titamenu.
Mtendere wambiri, pokutamandani
Mudziko lonseli, titamanu.