Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 44
  • Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tizigwira Ntchito Yokolola Mosangalala
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Kugaŵana Mokondwa m’Kututa
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Limbikirani ntchito yotuta!
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Sangalalani Ndi Ntchito Yotuta!
    Nsanja ya Olonda—2001
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 44

Nyimbo 44

Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala

Losindikizidwa

(Mateyo 13:1-23)

1. Tili munthawi yokolola,

Ndi mwayitu wapadera.

Okololawo ndi angelo

Nafe tikolole nawo.

Yesu watipatsa chitsanzo

Potitsogolera m’munda.

Ndi mwayidi womwe tapatsidwa

Kuchita nawo ntchitoyi.

2. Tikugwira nawo ntchitoyi

Pokonda M’lungu ndi m’nansi.

Ulaliki ndi kukolola

Zonse zili zofunika,

Ndife osangalala zedi

Pogwira ntchito ndi M’lungu.

Choncho tipirire pantchitoyi

M’lungu adzatidalitsa.

(Onaninso Mat. 24:13; 1 Akor. 3:9; 2 Tim. 4:2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena