Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 13
  • Pemphero Loyamikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pemphero Loyamikira
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Pemphero la Chiyamiko
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Pemphero Lothokoza
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Ufumu wa Yehova Wayamba Kulamulira
    Imbirani Yehova
  • Yehova Wayamba Kulamulira
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 13

Nyimbo 13

Pemphero Loyamikira

Losindikizidwa

(Salmo 95:2)

1. Yehova ndinu wachisomodi,

Muyeneratu kutamandidwa.

Tigwada kwa inu Womva pemphero,

Kuti inu mutisamalire.

Zolakwa zisonyeza uchimo,

Mutikhululukire machimo.

Munapereka dipo la Yesu.

Tipempha kuti mutiphunzitse.

2. Achimwemwe ndi oitanidwa

Mu bwalo lanu lolangizira.

Mutiphunzitsetu kukudziwani.

Tikonda kukhala m’nyumba yanu.

Dzanja lanu ndi lamphamvu kwambiri,

Lithandiza atumiki anu.

Tikutamanda Ufumu wanu.

Tiulalike, sudzalephera.

3. Tikondwa potisamala bwino,

Anthu onse alambire inu.

Ufumu wanu ndi wabwino zedi,

Udzachotsa matenda ndi imfa.

Mwana wanu adzachotsa zoipa,

Chilengedwe chidzasangalala.

Tiyeni tiimbe mothokoza:

“Titame Yehova Mfumu yathu!”

(Onaninso Sal. 65:2, 4, 11; Afil. 4:6.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena