Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 48
  • Timayenda ndi Yehova Tsiku Lililonse!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Timayenda ndi Yehova Tsiku Lililonse!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tiziyenda ndi Yehova Tsiku Lililonse
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Kuyenda ndi Yehova Masiku Onse
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kodi Muyenda ndi Mulungu?
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Muziyenda Ndi Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 48

Nyimbo 48

Timayenda ndi Yehova Tsiku Lililonse!

Losindikizidwa

(Mika 6:8)

1. Timayenda ndi Atate,

Nthawi zonse modzichepetsa.

N’ngokoma mtima kwa anthu

Ofunadi njira zakezo.

Afuna tiyende naye

Atatigwira dzanja.

Choncho tidzipereketu

Tikhale mbali ya M’lungu.

2. M’nthawi ya chiweruzoyi,

Pomwe dongosolo likutha,

Anthu otsutsa n’ngambiri

Omwe angamatiopseze

Yehova atiteteza,

Timuyandikirebe

Tim’tumikire kosatha

Tim’konde ndi mtima wonse.

3. M’lungu akutithandiza

Ndi mzimu ndi Mawu akenso

Watipatsa mpingo wake.

Amamvanso pemphero lathu

Tikayenda ndi Yehova

Tidzachita zabwino.

Tikhale okoma mtima

Ndiponso odzichepetsa.

(Onaninso Gen. 5:24; 6:9; 1 Maf. 2:3, 4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena