Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 135
  • Pirirani Mpaka pa Mapeto

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pirirani Mpaka pa Mapeto
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tipirire Mpaka Mapeto
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tipitirizebe Kupirira
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tipirirabe Mpaka Mapeto
    Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Pitirizanibe Kukhala M’gulu la Yehova
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 135

Nyimbo 135

Pirirani Mpaka pa Mapeto

Losindikizidwa

(Mateyu 24:13)

1. Zomwe M’lungu walonjeza,

Zomwe taphunzira

Zimatithandiza kukhala

Anthu opirira.

Usaiwale kuti

Tsikulo layandikira.

Mayesero akabwera

Ukhalebe wolimba.

2. Chikondi chako kwa M’lungu

Chisazilaretu,

Upirirebe,

Ngakhale m’mayesero a’kulu.

Usakayikire

Kapenatu kuchita mantha,

Yehova ali pafupi

Adzakupulumutsa.

3. Amene adzapirire

Mpakana mapeto

Ndiye adzapulumuke

Ndi kudzapeza moyo.

Lola kuti kupirira

Kugwire ntchito yake.

Yehova adzachititsa

Kuti usangalale.

(Onaninso Aheb. 6:19; Yak. 1:4; 2 Pet. 3:12; Chiv. 2:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena