Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 107
  • Bwerani Kuphiri la Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Bwerani Kuphiri la Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Bwerani Kuphiri la Yehova
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Kuyamikira Kudekha kwa Mulungu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 107

Nyimbo 107

Bwerani Kuphiri la Yehova

Losindikizidwa

(Yesaya 2:2-4)

1. Phiri la Yehova

Tangoliyang’anani,

Latalika kuposa

Ena onse lero.

Anthu akubwera

Kuchokera kutali,

Akuitanizana,

‘Bwerani kwa M’lungu.’

Tsopano wamng’ono

Wakhala mtundu waukulu.

Tikuona kuti

Tikudalitsidwa ndi M’lungu.

Ambiri tsopano

Akuvomerezadi

Ulamuliro wake

Mokhulupirika.

2. Yesu walamula

Kuti tipite ndithu

Tikalalikire

Uthenga wa Ufumu.

Khristu wayambano

Ulamuliro wake,

Ndipo akuti tikhale

Kumbali yake.

Ndi zosangalatsa

Kuona khamu lalikulu

Likukulirabe.

Ndipo tonse tikuthandiza.

Tonse tifuule

Anthu onsetu amve,

‘Bwerani anthuni

Kuphiri la Yehova.’

(Onaninso Sal. 43:3; 99:9; Yes. 60:22; Mac. 16:5.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena