Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsamba 2
  • N’chifukwa Chiyani Mumaona Kuti Kulambira Koyera N’kofunika?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Mumaona Kuti Kulambira Koyera N’kofunika?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • “Ili ndi Lamulo Lokhudza Kachisi”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Kulambira Koyera Kunabwezeretsedwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Lankhulani Chinenero Choyera ndi Kukhala ndi Moyo Kosatha!
    Nsanja ya Olonda—1991
  • “Yehova Mulungu Wako Ndi Amene Uyenera Kumulambira”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 September tsamba 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Mumaona Kuti Kulambira Koyera N’kofunika?

Masomphenya a Ezekieli okhudza kachisi analimbikitsa Ayuda amene anali ku ukapolo chifukwa anawapatsa chiyembekezo choti kulambira koyera kudzabwezeretsedwa. Masiku otsiriza ano, kulambira koyera ‘kwakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,’ ndipo ifeyo tili m’gulu la anthu a mitundu yonse omwe akhamukira kumeneko. (Yes. 2:2) Kodi mumasonyeza kuyamikira mwayi umene muli nawo wodziwa komanso kutumikira Yehova?

MADALITSO AMENE TIMAPEZA:

  • M’bale akuwerenga Baibulo

    Timalandira chakudya chauzimu chochuluka chomwe chimatithandiza kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri, malangizo otithandiza pa moyo komanso tikuyembekezera zinthu zabwino mtsogolo.​—Yes. 48:17, 18; 65:13; Aroma 15:4

  • Timasangalala ndi ubale wapadziko lonse.​—Sal. 133:1; Yoh. 13:35

  • Tili ndi mwayi wokhala antchito anzake a Mulungu pogwira nawo ntchito yolalikira imene sidzachitikanso.​—Mac. 20:35; 1 Akor. 3:9

  • Timakhala ndi “mtendere wa Mulungu” umene umatilimbikitsa pa nthawi ya mavuto.​—Afil. 4:6, 7

  • Timakhala ndi chikumbumtima choyera.​—2 Tim. 1:3

  • Timakhala pa “ubwenzi wolimba ndi Yehova.”​—Sal. 25:14

Kodi ndingasonyeze m’njira ziti kuti ndimaona kuti kulambira koyera n’kofunika?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena