Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsamba 4
  • Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Bungwe Lolamulira Limagwira Ntchito Bwanji Masiku Ano?
    Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova Masiku Ano?
  • Kodi Ndi Ndani Akutsogolera Anthu a Mulungu Masiku Ano?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Gulu Lowoneka la Mulungu
    Mungathe Kukhala ndi Moyo Kosatha m’Paradaiso pa Dziko Lapansi
  • “Tonse Tagwirizana”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 December tsamba 4
Mpingo wa m’nthawi ya atumwi ukumvetsera pamene kalata yochokera ku bungwe lolamulira ikuwerengedwa

Mpingo ukumvetsera malangizo ochokera ku bungwe lolamulira

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 15-16

Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu

Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani yokhudza mmene nkhani yamdulidwe inathetsedwera?

15:1, 2​—Tizikhala odzichepetsa komanso oleza mtima. M’malo mothetsa nkhaniyi okha, Paulo ndi Baranaba anapempha malangizo kuchokera ku gulu la Yehova.

15:28, 29​—Tizidalira gulu la Yehova. Mpingo unkakhulupirira kuti Yehova apitiriza kuutsogolera pogwiritsa ntchito mzimu woyera komanso Khristu Yesu.

16:4, 5​—Tizikhala omvera. Mipingo inapitiriza kukulirakulira pamene inkatsatira malangizo ochokera ku bungwe lolamulira.

Kodi ndi malangizo ati ochokera ku gulu la Yehova omwe tapatsidwa posachedwapa?

Kodi ineyo ndikupindula bwanji chifukwa chotsatira malangizowa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena