Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 102
  • “Muzithandiza Ofooka”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Muzithandiza Ofooka”
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • “Muthandize Ofookawo”
    Imbirani Yehova
  • ‘Muyenera Kuthandiza Ofookawo’
    Imbirani Yehova Zitamando
  • ‘Kondanani Wina ndi Mnzake’
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Kodi Mumaona Anthu Ofooka Mmene Yehova Amawaonera?
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 102

NYIMBO 102

“Muzithandiza Ofooka”

Losindikizidwa

(Machitidwe 20:35)

  1. 1. Tonse timavutika,

    Timafooka,

    Koma Mulungu wathu

    Amatikonda.

    Ali ndi chifundo

    Komanso chikondi.

    Nafe tikonde anthu,

    Tiwathandize.

  2. 2. Atumiki a M’lungu

    Angafooke.

    Tiziwalimbikitsa

    Ndi mawu athu.

    Mzimu wa Mulungu

    Umawalimbitsa.

    Tiziwadera nkhawa

    Tiwatonthoze.

  3. 3. M’malo mowaweruza

    Tikumbukire

    Kuti kukoma mtima

    N’kolimbikitsa.

    Tizichita khama

    Powalimbikitsa.

    Tikamawathandiza

    Amamva bwino.

(Onaninso Yes. 35:​3, 4; 2 Akor. 11:29; Agal. 6:2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena