Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
Moyo Wokhutiritsa Mmene Mungaupezere
Kosindikizidwa mu 2006
Kabuku kano kafalitsidwa monga mbali ya ntchito yophunzitsa anthu Baibulo yomwe ikuchitika padziko lonse. Ntchitoyi imayendetsedwa ndi zopereka zaufulu
Malemba onse m’kabuku kano achokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References
Kuyamikira Zithunzi
Tsamba 12: Chithunzi cha NASA; tsamba 13: Pamwamba: HUC, Tel Dan Excavations; chithunzi: Zeev Radovan; m’munsi: Mwa chilolezo cha American Numismatic Society, New York; tsamba 15: M’mwamba: Culver Pictures; pakatipo: © Nobelstiftelsen; m’munsi: Mwa chilolezo cha Anglo-Australian Observatory, wojambula: David Malin; tsamba 17: Kompyuta yotsogola kwambiri: Mwa chilolezo cha Sandia National Laboratories; tsamba 18: Malemba achihebri: © John C. Trever; tsamba 25: UN PHOTO 148051/J.P. Laffont–SYGMA; tsamba 30: Utsi wa bomba la Atomu: Chithunzi cha USAF; asilikali: Chithunzi cha U.S. Marine Corps; ana anjala: WHO/OXFAM