Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 56
  • Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
    Imbirani Yehova
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Moyo Wosatha Ulonjezedwa
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 56

NYIMBO 56

Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha

Losindikizidwa

(Miyambo 3:​1, 2)

  1. 1. Kukonda choonadi ndikofunika,

    Wina sangakusankhireni.

    Muzimvera malangizo a Mulungu

    Ndi kumukhulupirira.

    (KOLASI)

    Muzichikonda

    Choonadi panokha

    Ndipo muzikhala

    Ndi chimwemwe

    Mukamachikondadi.

  2. 2. Mukamatumikira M’lungu mwakhama,

    Mudzalandira madalitso

    Komanso mudzapeza moyo wosatha,

    Wamtendere ndi wabwino.

    (KOLASI)

    Muzichikonda

    Choonadi panokha

    Ndipo muzikhala

    Ndi chimwemwe

    Mukamachikondadi.

  3. 3. M’maso mwa M’lungu tilitu ngati ana

    Ofunika kulangizidwa.

    Tiziyenda ndi Atate wakumwamba

    Ndipo tidzadalitsidwa.

    (KOLASI)

    Muzichikonda

    Choonadi panokha

    Ndipo muzikhala

    Ndi chimwemwe

    Mukamachikondadi.

(Onaninso Sal. 26:3; Miy. 8:35; 15:31; Yoh. 8:​31, 32.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena