Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 41
  • Imvani Pemphero Langa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Imvani Pemphero Langa
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Mulungu Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova
  • Yehova, Nyonga Yathu ndi Mphamvu Yathu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • M’patseni Yehova Ulemerero
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Umsenze Yehova Nkhaŵa Zako
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 41

NYIMBO 41

Imvani Pemphero Langa

Losindikizidwa

(Salimo 54)

  1. 1. Atate mumve pempheroli.

    M’lungu wanga ine ndi wanu.

    Ndidzatamanda dzina lanu.

    (KOLASI)

    Yehova mumve pempheroli.

  2. 2. Ndathokoza mphatso ya moyo.

    Mumandisamalira ndithu.

    Mumandithandiza mu zonse.

    (KOLASI)

    Yehova mumve pempheroli.

  3. 3. Ndizichita zinthu zabwino.

    Ndiyende mukuwala kwanu.

    Ndipirire mavuto onse.

    (KOLASI)

    Yehova mumve pempheroli.

(Onaninso Eks. 22:27; Sal. 106:4; Yak. 5:​11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena