Zimene Zili M’bukuli
Mutu
1 “Taonani! Uyu Ndi Mulungu Wathu” 7
2 Kodi N’zothekadi ‘Kuyandikira Mulungu’? 16
3 “Woyera, Woyera, Woyera Ndi Yehova” 26
4 ‘Yehova Ali Ndi Mphamvu Zambiri’ 37
5 Mphamvu za Kulenga—‘Anapanga Kumwamba Komanso Dziko Lapansi’ 47
6 Mphamvu Zowononga—“Yehova Ndi Msilikali Wamphamvu” 57
7 Mphamvu Zoteteza—“Mulungu Ndi Pothawira Pathu” 67
8 Mphamvu Zobwezeretsa—Yehova ‘Akupanga Zinthu Zonse Kuti Zikhale Zatsopano’ 77
9 “Khristu Ndi Mphamvu ya Mulungu” 87
10 “Muzitsanzira Mulungu” Mukamagwiritsa Ntchito Mphamvu 97
GAWO 2—“Yehova Amakonda Chilungamo”
11 “Njira Zake Zonse Ndi Zolungama” 108
12 “Kodi Mulungu Alibe Chilungamo?” 118
13 ‘Malamulo a Yehova Ndi Angwiro’ 128
14 Yehova Anapereka “Dipo Kuti Awombole Anthu Ambiri” 138
15 Yesu ‘Akukhazikitsa Chilungamo Padziko Lapansi’ 148
16 ‘Muzichita Chilungamo’ Poyenda ndi Mulungu 158
GAWO 3—“Ali Ndi Mtima Wanzeru”
17 ‘Nzeru za Mulungu N’zozama’ 169
18 “Mawu a Mulungu” Amasonyeza Kuti Iye Ndi Wanzeru 179
19 ‘Nzeru ya Mulungu Imaonekera mu Chinsinsi Chopatulika’ 189
20 “Ali ndi Mtima Wanzeru” Koma Ndi Wodzichepetsa 199
21 Yesu Amatisonyeza “Nzeru za Mulungu” 209
22 Kodi Mumagwiritsa Ntchito “Nzeru Yochokera Kumwamba”? 219
GAWO 4—“Mulungu Ndi Chikondi”
23 “Mulungu Ndi Amene Anayamba Kutikonda” 231
24 Palibe Chimene ‘Chingatisiyanitse ndi Chikondi cha Mulungu’ 240
25 “Chifundo Chachikulu cha Mulungu Wathu” 250
26 Mulungu “Wokonzeka Kukhululuka” 260
27 “Ubwino Wake Ndi Waukulu Kwambiri!” 270
28 ‘Inu Nokha Ndinu Wokhulupirika’ 280
29 “Mudziwe Chikondi cha Khristu” 290