Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g05 12/8 tsamba 32
  • Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!
  • Galamukani!—2005
  • Timitu
  • ACHINYAMATA AKUFUNSA
  • CHIPEMBEDZO
  • CHUMA NDI NTCHITO
  • MAUNANSI A ANTHU
  • MAYIKO NDI ANTHU
  • MBONI ZA YEHOVA
  • NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
  • SAYANSI
  • UMOYO NDI MANKHWALA
  • ZIMENE BAIBULO LIMANENA
  • ZINYAMA NDI ZOMERA
  • ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
  • ZOSIYANASIYANA
Galamukani!—2005
g05 12/8 tsamba 32

Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!

ACHINYAMATA AKUFUNSA

Anthu Ena Akandiuza Mavuto Awo, 2/8

Kucheza ndi Anthu Olakwika, 8/8, 9/8

Kucheza ndi Anthu pa Intaneti, 10/8, 11/8

Kupeza Chibwenzi pa Intaneti, 5/8, 6/8

Ndingatani Kuti Ndiziugwira Mtima? 3/8

Ndingatani Mnyamata Amene Ndimamufuna Akandikana? 1/8

Ndingatani Ngati Mtsikana Akundifuna? 7/8

Ndizigwira Ntchito Yamanja Chifukwa Chiyani? 4/8

Tichite Kukhala ndi Mwambo Wonse wa Ukwati? 12/8

CHIPEMBEDZO

Kodi Yesu Kristu Ndi Mulungu? 5/8

CHUMA NDI NTCHITO

Kupeza ndi Kukhalitsa Pantchito, 7/8

MAUNANSI A ANTHU

Amayi Ndi Aphunzitsi, 3/8

Kukongola Kofunika Kwambiri, 1/8

Kumvetsa Mavuto Amene Dokotala Wanu Akukumana Nawo, 2/8

Kuthandiza Achinyamata Amene Ali Pamavuto, 4/8

MAYIKO NDI ANTHU

Chigwa cha Ngorongoro (Tanzania), 1/8

Malo Ovuta Kuwamvetsa a ku Africa, 11/08

“Ndinu Dr. Livingstone, Eti?” (Tanzania), 2/8

Nyanja ya Pinki (Senegal), 10/8

“Palibe Mawu Otukwana” (mtundu wa Apache), 7/8

“Tikakumane Pachitsime” (Moldova), 11/8

MBONI ZA YEHOVA

Achinyamata Amalalikira Mogwira Mtima, 9/8

Kupereka Umboni Wabwino ku Sukulu (Mexico), 10/8

Kusintha Akaidi, 4/8

Mulungu Amalemekezeka Tikamachita Zinthu Moona Mtima, 9/8

“Muzinyadira Zimenezi,” 6/8

Ndende za ku Mexico, 10/8

“Ndikanakonda Anthu Akanadziwa Zimenezi!” (Dominican Republic), 1/8

Nkhani Yakale Inakhudza Mitima ya Anthu, 8/8

NKHANI ZA MOYO WA ANTHU

Kukopeka ndi Mlengi Chifukwa cha Kukongola kwa Choonadi (T. Fujii), 8/8

Kwalembedwa Kuti Ndidzawaonanso (R. Phillips), 1/8

Ndinafunitsitsa Kukwanitsa Cholinga Changa (M. Serna), 7/8

Ndinatha Kutumikira Mulungu Ngakhale Zinali Zovuta (I. Mikitkov), 5/8

Nkhondo Imene Inasintha Moyo Wanga (M. Molina), 11/8

Sayansi ndi Baibulo Zinandithandiza Kudziwa Cholinga cha Moyo (B. Oelschlägel), 12/8

Tinapeza Chinachake Chabwino Koposa (F. Del Rosario de Páez), 9/8

Wokonzeka Kuthandiza Ena (C. Vavy), 3/8

Zilema Zanga Sizinandifooketse (K. N’Guessan), 12/8

SAYANSI

Dzuwa Kuwala Pakati pa Usiku, 6/8

UMOYO NDI MANKHWALA

Khansa Yapakhungu, 6/8

Kuchita Zinthu Zolimbitsa Thupi, 6/8

Kumvetsa Mavuto Amene Dokotala Wanu Akukumana Nawo, 2/8

Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso, 10/8

Moyo Wopanikizika, 2/8

Utsi Wakupha (wa nkhuni), 6/8

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Akazi Azibisa Kukongola Kwawo? 10/8

Kodi Baibulo Limapondereza Akazi? 11/8

Kodi Kufatsa N’kupanda Mphamvu? 1/8

Kodi Kufuna Kutchuka N’kulakwa? 6/8

Kodi Mulungu Ali Paliponse? 3/8

Kodi Mulungu Amakondera Mitundu Ina ya Anthu? 12/8

Kodi Muyenera Kuopa Armagedo? 7/8

Kodi Nyenyezi Zingakuthandizeni Kudziwa Tsogolo Lanu? 8/8

Kugwiritsa Ntchito Zithunzi Popemphera, 5/8

Kupatsa Ana Chisamaliro Chimene Amafunikira, 2/8

Kupemphera kwa Mariya Virigo? 9/8

Maukwati a Amuna Okhaokha Kapena Akazi Okhaokha, 4/8

ZINYAMA NDI ZOMERA

Mgwirizano, 9/8

Tomato, 3/8

ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE

Dziko Likusakazidwa Kwabasi, 1/8

Kuba M’masitolo, 7/8

Kudyetsa Anthu Wani Biliyoni, 8/8

Kukhala Mopanda Mantha, 8/8

Kupezera Chakudya Anthu Okhala M’mizinda, 12/8

Kusowa Pokhala, 12/8

Mafilimu, 5/8

Masoka Achilengedwe, 8/8

Mmene Mungapindulire ndi Manyuzipepala, 11/8

Msampha wa Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso, 10/8

Njira Zosawononga Dziko Zopangira Magetsi, 3/8

Ntchito Zokopa Alendo, 9/8

Vuto la Padziko Lonse la Kusowa kwa Nyumba, 10/8

Zimene Osauka Angayembekezere, 11/8

ZOSIYANASIYANA

Mafoni a M’manja Ndi Abwino Kapena Ndi Oipa? 2/8

Mapiri Ndi Ofunika kwa Zamoyo, 4/8

Mumayendetsa Galimoto Mbali Iti ya Msewu? 4/8

Pakhomo Paukhondo, 6/8

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena