Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 5/07 tsamba 32
  • Kodi Ndani Ali Otsatira Oona a Khristu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Ndani Ali Otsatira Oona a Khristu?
  • Galamukani!—2007
Galamukani!—2007
g 5/07 tsamba 32

Kodi Ndani Ali Otsatira Oona a Khristu?

Kuti mudziwe yankho la funso lochititsa chidwili, tikukuitanani ku Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova wakuti “TSATIRANI KHRISTU!”

Padziko lonse padzachitika misonkhano yambirimbiri yotereyi ndipo idzayamba m’mwezi wa May, ku United States. Kuti mudziwe malo a kufupi ndi kwanu amene kukachitikire msonkhanowu, funsani Mboni za Yehova kwanuko kapena tilembereni kalata. Magazini ya Nsanja ya Olonda (yomwe ndi inzake ya magazini ino) ya March 1, 2007, ili ndi mndandanda wa malo onse amene kukachitikire msonkhanowu ku Malawi ndi ku Mozambique.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena