Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 9/08 tsamba 13-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi pa Chithunzichi Pakusowa Chiyani?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 9/08 tsamba 13-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi pa Chithunzichi Pakusowa Chiyani?

Werengani Chivumbulutso 12:3. Tsopano yang’anani pa chithunzicho. Kodi ndi zinthu ziti zimene zikusowapo? Lembani mayankho anu m’mizere ili m’munsiyi, ndipo malizitsani kujambula zinthu zimene zikusowazo.

1. ․․․․․

2. ․․․․․

3. ․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi chinjoka chimenechi chikuimira ndani? Kodi iye akuchita chiyani ndi dziko lonse lapansi kumene kuli anthu?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Chivumbulutso 12:9.

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

TSAMBA 3 Kodi Mulungu waika chiyani m’maganizo ndi m’mitima ya anthu? Mlaliki 3:․․․

TSAMBA 5 Kodi Mulungu amapereka mphatso yotani? Aroma 6:․․․

TSAMBA 21 Kodi ndi mayina aulemu komanso achipembedzo otani amene Yesu ananena kuti tisamagwiritse ntchito? Mateyo 23:․․․

TSAMBA 27 Kodi munthu wochenjera amatani? Miyambo 22:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?

Onani zokuthandizani kupeza yankho. Onaninso malembawo. Kenaka lembani mayina olondola pa mizereyi.

4. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Zera Mkusi pamodzi ndi amuna 1 miliyoni anandiukira koma Yehova anawakantha pamaso panga.

Werengani 2 Mbiri 14:9-12.

5. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinakonza zakuti Chilamulo cha Yehova chiphunzitsidwe m’midzi ya Yuda.

Werengani 2 Mbiri 17:1, 7-9.

6. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinaikidwa m’manda a m’Mudzi wa Davide koma osati m’manda a mafumu.

Werengani 2 Mbiri 21:16-20.

◼ Mayankho ali pa tsamba 13

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Mutu umodzi ndi khosi limodzi.

2. Nyanga 10.

3. Zisoti zachifumu 7.

4. Asa.—Mateyo 1:7.

5. Yehosafati.—Mateyo 1:8. 6.

6. Yehoramu.—Mateyo 1:8.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena